Macitidwe 5:15 BL92

15 kotero kuti ananyamulanso naturuka nao odwala Ifumakwalala, nawaika pamakama ndi pamphasa, kuti, popita Petro, ngakhale cithunzi cace cigwere wina wa iwo.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 5

Onani Macitidwe 5:15 nkhani