16 Komanso unasonkhana pamodzi unyinji wa anthu ocokera ku midzi yozungulira Yerusalemu, alikutenga odwala, ndi obvutika ndi mizimu yonyansa; ndipo anaciritsidwa onsewa.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 5
Onani Macitidwe 5:16 nkhani