2 Ndipo khumi ndi awiriwo anaitana unyinji wa ophunzira, nati, Sikuyenera kuti ife tisiye mau a Mulungu ndi kutumikira podyerapo.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 6
Onani Macitidwe 6:2 nkhani