1 Koma masiku awo, pakucurukitsa ophunzira, kunauka cidandaulo, Aheleniste kudandaula pa Ahebri, popeza amasiye ao anaiwalika pa citumikiro ca tsiku ndi tsiku.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 6
Onani Macitidwe 6:1 nkhani