7 Ndipo mau a Mulungu anakula; ndipo ciwerengero ca akuphunzira cidacurukatu ku Yerusalemu; ndipo khamu lalikuru la ansembe linamvera cikhulupiriroco.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 6
Onani Macitidwe 6:7 nkhani