10 namlanditsa iye m'zisautso zace zonse, nampatsa cisomo ndi nzeru pamaso pa Farao mfumu ya ku Aigupto; ndipo anamuika iye kazembe wa pa Aigupto ndi pa nyumba yace yonse.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7
Onani Macitidwe 7:10 nkhani