11 Koma inadza njala pa Aigupto ndi Kanani lonse, ndi cisautso cacikuru; ndipo sanapeza cakudya makolo athu.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7
Onani Macitidwe 7:11 nkhani