Macitidwe 7:8 BL92

8 Ndipo anaiupatsa iye cipangano ca mdulidwe; ndipo kotero Abrahamu anabala Isake, namdula tsiku lacisanu ndi citatu; ndi Isake anabala Yakobo, ndi Yakobo anabala makolo akulu aja khumi ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 7

Onani Macitidwe 7:8 nkhani