Macitidwe 8:25 BL92

25 Pamenepo iwo, atatha kucita umboni ndi kulankhula mau a Ambuye, anabwerakunkaku Yerusalemu, nalalikira Uthenga Wabwi no ku midzi yambirl ya Asamariya.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 8

Onani Macitidwe 8:25 nkhani