Macitidwe 8:26 BL92

26 Koma mngelo wa Ambuye analankhula ndi Filipo, nanena, Nyamuka, nupite mbali ya kumwela, kutsata njira yotsika kucokera ku Yerusalemu kunka ku Gaza; ndiyo ya cipululu.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 8

Onani Macitidwe 8:26 nkhani