40 Koma Filipo anapezedwa ku Azotu; ndipo popitapitaanalalikira Uthenga Wabwino m'midzi yonse, kufikira anadza iye ku Kaisareya.
Werengani mutu wathunthu Macitidwe 8
Onani Macitidwe 8:40 nkhani