Macitidwe 9:38 BL92

38 Ndipo popeza Luda ndi pafupi pa Yopa, m'mene anamva ophunzirawo kuti Petro anali pomwepo, anamtumizira anthu awiri, namdandaulira, Musacedwa mudze kwa ife.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 9

Onani Macitidwe 9:38 nkhani