Macitidwe 9:39 BL92

39 Ndipo Petro anayamuka, napita nao. M'mene anafikako, anapita naye ku cipinda ca pamwamba; ndipo amasiye onse anaimirirapo pali iye, nalira, namuonetsa maraya ndizobvala zimene Dorika adasoka, pamene anali nao pamodzi.

Werengani mutu wathunthu Macitidwe 9

Onani Macitidwe 9:39 nkhani