1 Mbiri 19:4 BL92

4 Ndipo Hanuni anatenga anyamata a Davide, nawameta, nadula malaya ao pakati kufikira m'matako, nawaleka acoke.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 19

Onani 1 Mbiri 19:4 nkhani