2 Mbiri 1:1 BL92

1 NDIPO Solomo mwana wa Davide analimbikitsidwa m'ufumu wace, ndipo Yehova Mulungu wace anali naye, namkuza kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 1

Onani 2 Mbiri 1:1 nkhani