2 Mbiri 1:4 BL92

4 Koma likasa la Mulungu Davide adakwera nalo kucokera ku Kiriyati Yearimu kumka kumene Davide adalikonzeratu malo; pakuti adaliutsiratu hema ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 1

Onani 2 Mbiri 1:4 nkhani