2 Mbiri 1:7 BL92

7 Usiku womwewo Mulungu anaonekera kwa Solomo, nati kwa iye, Pempha comwe ndikupatse.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 1

Onani 2 Mbiri 1:7 nkhani