15 Momwemo mfumu siinamvera anthuwo; pakuti kusinthaku kudafuma kwa Mulungu, kuti Yehova akhazikitse mau ace, amene ananenetsa Ahiya wa ku Silo kwa Yerobiamu mwana wa Nebati.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 10
Onani 2 Mbiri 10:15 nkhani