2 Ndipo kunali, atamva Yerobiamu mwana wa Nebati (popeza anali m'Aigupto kumene adathawira, kuthawa Solomo mfumu), Yerobiamu anabwera kucoka ku Aigupto.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 10
Onani 2 Mbiri 10:2 nkhani