2 Mbiri 11:1 BL92

1 Ndipo atafika ku Yerusalemu Rehabiamu, anamemeza a nyumba ya Yuda ndi Benjamini amuna osankhika zikwi zana limodzi mphambu makumi asanu ndi atatu, ndiwo ankhondo, alimbane ndi Aisrayeli kubwezanso ufumu kwa Rehabiamu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 11

Onani 2 Mbiri 11:1 nkhani