2 Mbiri 11:22 BL92

22 Ndipo Rehabiamu anaika Abiya mwana wa Maaka akhale wamkuru, kalonga mwa abale ace; ndiko kuti adzamlonga ufumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 11

Onani 2 Mbiri 11:22 nkhani