11 Ndipo kunatero kuti pakulowa mfumu m'nyumba ya Yehova, anadza olindirira, nazinyamula, nazibwezanso ku cipinda ca olindirira.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 12
Onani 2 Mbiri 12:11 nkhani