15 Pamenepo amuna a Yuda anapfuula cokweza; ndipo popfuula amuna a Yuda, kunacitika kuti Mulungu anakantha Yerobiamu ndi Aisrayeli onse pamaso pa Abiya ndi Yuda.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 13
Onani 2 Mbiri 13:15 nkhani