2 Mbiri 13:5 BL92

5 simudziwa kodi kuti Yehova Mulungu wa Israyeli anapereka ciperekere ufumu wa Israyeli kwa Davide, kwa iye ndi ana ace, ndi pangano la mcere?

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 13

Onani 2 Mbiri 13:5 nkhani