2 Mbiri 14:1 BL92

1 Momwemo Abiya anagona ndi makolo ace, ndipo anamuika m'mudzi wa Davide; ndi Asa mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace, m'masiku ace dziko linaona bata zaka khumi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 14

Onani 2 Mbiri 14:1 nkhani