2 Mbiri 14:8 BL92

8 Ndipo Asa anali nao ankhondo ogwira zikopa ndi mikondo, a m'Yuda zikwi mazana atatu; ndi a m'Benjamini ogwira malihawo ndi okoka mauta zikwi mazana awiri mphambu makumi asanu ndi atatu; onsewo ngwazi zamphamvu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 14

Onani 2 Mbiri 14:8 nkhani