2 Mbiri 15:16 BL92

16 Maaka yemwe, mai wace wa Asa, mfumu, anamcotsa uyu asakhalenso mai wa ufumu, popeza anapanga fano loopsa la Asera; ndipo Asa analikha fano lace, naliphwanyaphwanya, nalitenthera ku mtsinje wa Kedroni.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 15

Onani 2 Mbiri 15:16 nkhani