2 Mbiri 15:8 BL92

8 Ndipo pakumva Asa mau awa, ndi cinenero ca Odedi mneneriyo, analimbika mtima, nacotsa zonyansazo m'dziko lonse la Yuda ndi Benjamini, ndi m'midzi adailanda ku mapiri a Efraimu; nakonza guwa la nsembe la Yehova lokhala pakhomo pa likole la Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 15

Onani 2 Mbiri 15:8 nkhani