2 Mbiri 16:4 BL92

4 Ndipo Benihadadi anamvera mfumu Asa natumiza akazembe a magulu ace a nkhondo ayambane ndi midzi ya Israyeli, nakantha Iyoni, ndi Dani, ndi Abelimaimu, ndi midzi yonse ya cuma ya Nafitali,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 16

Onani 2 Mbiri 16:4 nkhani