2 Mbiri 16:6 BL92

6 Pamenepo Asa mfumu anatenga Ayuda onse, ndipo anatuta miyala ya ku Rama, ndi mitengo yace, imene Basa adamanga nayo, namangira Geba ndi Mizipa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 16

Onani 2 Mbiri 16:6 nkhani