2 Mbiri 17:14 BL92

14 Kuwerenga kwao monga mwa nyumba za atate ao ndiko: a Yuda, akuru a zikwi; Adina wamkuru, ndi pamodzi ndi iye ngwazi zamphamvu zikwi mazana atatu;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 17

Onani 2 Mbiri 17:14 nkhani