2 Mbiri 17:2 BL92

2 Naika ankhondo m'midzi yonse yamalinga ya Yuda, naika aboma m'dziko la Yuda, ndi m'midzi ya Efraimu, imene adailanda Asa atate wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 17

Onani 2 Mbiri 17:2 nkhani