8 Yehosafati anaikanso m'Yerusalemu Alevi, ndi ansembe ena, ndi akuru a nyumba za makolo m'Israyeli, aweruzire Yehova, nanene mirandu. Ndipo anabwerera kudza ku Yerusalemu.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 19
Onani 2 Mbiri 19:8 nkhani