2 Mbiri 23:17 BL92

17 Ndi anthu onse anamuka ku nyumba ya Baala, naipasula, naphwanya maguwa ace a nsembe, ndi mafano ace; namupha Matana wansembe wa Baala ku maguwa a nsembe.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 23

Onani 2 Mbiri 23:17 nkhani