1 Yoasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mace ndiye Zibiya wa ku Beereseba.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 24
Onani 2 Mbiri 24:1 nkhani