2 Mbiri 24:15 BL92

15 Koma Yehoyada anakalamba, nacuruka masiku, namwalira iye; ndiye wa zaka zana limodzi mphambu makumi atatu pamene anamwalira.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 24

Onani 2 Mbiri 24:15 nkhani