2 Mbiri 25:17 BL92

17 Pamenepo Amaziya mfumu ya Yuda anafunsana ndi ompangira, natumiza kwa Yoasi mwana wa Yehoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Israyeli, ndi kuti, Idzani, tionane maso.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:17 nkhani