19 Mukuti, Taonani, ndakantha Aedomu, nukwezeka mtima wanu kudzikuza; khalani kwanu tsopano, mungadziutsire tsoka, mungagwe, inu, ndi Yuda pamodzi ndi inu.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25
Onani 2 Mbiri 25:19 nkhani