2 Mbiri 25:24 BL92

24 Natenga golidi ndi siliva zonse, ndi zipangizo zonse zopezeka m'nyumba ya Mulungu kwa Obedi Edomu, ndi cuma ca nyumba ya mfumu, acikole omwe; nabwerera kumka ku Samariya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:24 nkhani