2 Mbiri 26:16 BL92

16 Koma atakhala wamphamvu, mtima wace unakwezeka momuononga, nalakwira Yehova Mulungu wace; popeza analowa m'Kacisi wa Yehova kufukiza pa guwa la nsembe la cofukiza.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 26

Onani 2 Mbiri 26:16 nkhani