2 Mbiri 26:20 BL92

20 Ndipo Azariya wansembe wamkulu, ndi ansembe onse, anampenya, ndi kuona kuti anali wakhate pamphumi pace namkankhiza msanga kubwalo; nafulumiranso yekha kuturukako, pakuti Yehova adamkantha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 26

Onani 2 Mbiri 26:20 nkhani