2 Mbiri 28:24 BL92

24 Ndipo Ahazi anasonkhanitsa zipangizo za m'nyumba ya Mulungu, naduladula zipangizo za m'nyumba ya Mulungu, natseka pa makomo a nyumba ya Yehova, nadzimangira maguwa a nsembe m'ngondya ziri zonse za Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 28

Onani 2 Mbiri 28:24 nkhani