6 Pakuti Peka mwana wa Remaliya anapha ku Yuda tsiku limodzi zikwi zana limodzi ndi makumi awiri, ngwazi zonsezo; popeza adasiya Yehova Mulungu wa makolo ao.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 28
Onani 2 Mbiri 28:6 nkhani