2 Mbiri 28:8 BL92

8 Ndipo ana a Israyeli anatenga ndende ena a abale ao zikwi mazana awiri, akazi, ana amuna ndi akazi, nalandanso kwa iwo zofunkha zambiri, nabwera nazo zofunkhazo ku Samariya,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 28

Onani 2 Mbiri 28:8 nkhani