2 Mbiri 29:12 BL92

12 Pamenepo ananyamuka Alevi, Mahati mwana wa Amasai ndi Yoeli mwana wa Azariya, a ana a Akohati; ndi a ana a Merari, Kisi mwana wa Abidi, ndi Azariya mwana wa Yehaleleli; ndi a Agerisoni, Yowa mwana wa Zima, ndi Edeni mwana wa Yowa;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:12 nkhani