2 Mbiri 29:15 BL92

15 Ndipo anamemeza abale ao, nadzipatula, nalowa monga adawauza mfumu mwa mau a Yehova, kuyeretsa nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:15 nkhani