2 Mbiri 29:22 BL92

22 Momwemo anapha ng'ombezo, ndi ansembe analandira mwazi, nauwaza pa guwa la nsembe, napha nkhosa zamphongozo, nawaza mwazi pa guwa la nsembe; anaphanso ana a nkhosawo, nawaza mwazi pa guwa la nsembe.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:22 nkhani