2 Mbiri 29:27 BL92

27 Nanena Hezekiya kuti apereke nsembe yopsereza pa guwa la nsembe. Ndipo pakuyamba nsembe yopsereza, inayambanso nyimbo ya Yehova ndi malipenga, pamodzi ndi zoyimbira za Davideyo mfumu ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:27 nkhani