30 Hezekiya mfumu ndi akalonga anauzanso Alevi ayimbire Yehova zomlemekeza ndi mau a Davide ndi a Asafu mlauli. Ndipo anayimbira zomlemekeza mokondwera, nawerama mitu yao, nalambira.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29
Onani 2 Mbiri 29:30 nkhani