2 Mbiri 3:13 BL92

13 Mapiko a akerubi awa anafunyululika mikono makumi awiri; ndipo anaima ndi mapazi ao, ndi, nkhope zao zinaloza kukhomo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 3

Onani 2 Mbiri 3:13 nkhani